Daily Manna for Friday, October 30, 2020

Daily Manna is a daily Bible devotional service provided by Biblica. The Scripture is provided in many forms and is new every day. It is a great way to receive the encouragement and hope found in the Word of God.

Verse of the Day

Deuteronomo 28:1-6

Ngati mumvera Yehova Mulungu wanu ndi kutsatira mosamalitsa malamulo ake onse amene ndikukupatsani lero lino, Yehova Mulungu wanu adzakukwezani pamwamba pa mitundu yonse ya pa dziko lapansi. Madalitso awa adzabwera kwa inu ndi kuyenda nanu ngati mumvera Yehova Mulungu wanu:

Mudzadalitsika mʼmizinda yanu ndi kudalitsika mʼdzikolo.

Yehova adzadalitsa ana anu, zokolola za mʼdziko lanu, ngʼombe zanu pamodzi ndi ziweto zanu zonse.

Dengu lanu ndi chiwaya chanu cha buledi zidzadalitsika.

Mudzadalitsika pa kulowa kwanu ndi pa kutuluka kwanu.