1 Chronicles 8 – NIV & CCL

New International Version

1 Chronicles 8:1-40

The Genealogy of Saul the Benjamite

1Benjamin was the father of Bela his firstborn,

Ashbel the second son, Aharah the third,

2Nohah the fourth and Rapha the fifth.

3The sons of Bela were:

Addar, Gera, Abihud,8:3 Or Gera the father of Ehud 4Abishua, Naaman, Ahoah, 5Gera, Shephuphan and Huram.

6These were the descendants of Ehud, who were heads of families of those living in Geba and were deported to Manahath:

7Naaman, Ahijah, and Gera, who deported them and who was the father of Uzza and Ahihud.

8Sons were born to Shaharaim in Moab after he had divorced his wives Hushim and Baara. 9By his wife Hodesh he had Jobab, Zibia, Mesha, Malkam, 10Jeuz, Sakia and Mirmah. These were his sons, heads of families. 11By Hushim he had Abitub and Elpaal.

12The sons of Elpaal:

Eber, Misham, Shemed (who built Ono and Lod with its surrounding villages), 13and Beriah and Shema, who were heads of families of those living in Aijalon and who drove out the inhabitants of Gath.

14Ahio, Shashak, Jeremoth, 15Zebadiah, Arad, Eder, 16Michael, Ishpah and Joha were the sons of Beriah.

17Zebadiah, Meshullam, Hizki, Heber, 18Ishmerai, Izliah and Jobab were the sons of Elpaal.

19Jakim, Zikri, Zabdi, 20Elienai, Zillethai, Eliel, 21Adaiah, Beraiah and Shimrath were the sons of Shimei.

22Ishpan, Eber, Eliel, 23Abdon, Zikri, Hanan, 24Hananiah, Elam, Anthothijah, 25Iphdeiah and Penuel were the sons of Shashak.

26Shamsherai, Shehariah, Athaliah, 27Jaareshiah, Elijah and Zikri were the sons of Jeroham.

28All these were heads of families, chiefs as listed in their genealogy, and they lived in Jerusalem.

29Jeiel8:29 Some Septuagint manuscripts (see also 9:35); Hebrew does not have Jeiel. the father8:29 Father may mean civic leader or military leader. of Gibeon lived in Gibeon.

His wife’s name was Maakah, 30and his firstborn son was Abdon, followed by Zur, Kish, Baal, Ner,8:30 Some Septuagint manuscripts (see also 9:36); Hebrew does not have Ner. Nadab, 31Gedor, Ahio, Zeker 32and Mikloth, who was the father of Shimeah. They too lived near their relatives in Jerusalem.

33Ner was the father of Kish, Kish the father of Saul, and Saul the father of Jonathan, Malki-Shua, Abinadab and Esh-Baal.8:33 Also known as Ish-Bosheth

34The son of Jonathan:

Merib-Baal,8:34 Also known as Mephibosheth who was the father of Micah.

35The sons of Micah:

Pithon, Melek, Tarea and Ahaz.

36Ahaz was the father of Jehoaddah, Jehoaddah was the father of Alemeth, Azmaveth and Zimri, and Zimri was the father of Moza. 37Moza was the father of Binea; Raphah was his son, Eleasah his son and Azel his son.

38Azel had six sons, and these were their names:

Azrikam, Bokeru, Ishmael, Sheariah, Obadiah and Hanan. All these were the sons of Azel.

39The sons of his brother Eshek:

Ulam his firstborn, Jeush the second son and Eliphelet the third. 40The sons of Ulam were brave warriors who could handle the bow. They had many sons and grandsons—150 in all.

All these were the descendants of Benjamin.

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mbiri 8:1-40

Adzukulu a Benjamini ndi Sauli

1Benjamini anabereka Bela mwana wake woyamba,

wachiwiri Asibeli, wachitatu Ahara,

2wachinayi Noha ndipo wachisanu Rafa.

3Ana a Bela anali awa:

Adari, Gera, Abihudi, 4Abisuwa, Naamani, Ahowa, 5Gera, Sefufani ndi Hiramu.

6Zidzukulu za Ehudi, zimene zinali atsogoleri a mabanja a amene amakhala ku Geba ndipo zinasamutsidwa kupita ku Manahati zinali izi:

7Naamani, Ahiya ndi Gera, amene anawasamutsa ndipo anabereka Uza ndi Ahihudi.

8Saharaimu anabereka ana ku Mowabu atalekana ndi akazi ake, Husimu ndi Baara. 9Mwa mkazi wake Hodesi anabereka Yobabu, Zibiya, Mesa, Malikamu, 10Yeusi, Sakiya ndi Mirima. Awa ndiye ana ake, atsogoleri a mabanja awo. 11Mwa mkazi wake Husimu anabereka Abitubi ndi Elipaala.

12Ana a Elipaala anali awa:

Eberi, Misamu, Semedi (amene anamanga mizinda ya Ono ndi Lodi ndi midzi yake yozungulira) 13ndiponso Beriya ndi Sema, amene anali atsogoleri a mabanja a amene ankakhala ku Ayaloni ndipo anathamangitsa nzika za ku Gati.

14Ahiyo, Sasaki, Yeremoti, 15Zebadiya, Aradi, Ederi, 16Mikayeli, Isipa ndi Yoha anali ana a Beriya.

17Zebadiya, Mesulamu, Hiziki, Heberi, 18Isimerai, Iziliya ndi Yobabu anali ana a Elipaala.

19Yakimu, Zikiri, Zabidi, 20Elienai, Ziletai, Elieli, 21Adaya, Beraya ndi Simirati anali ana a Simei.

22Isipani, Eberi, Elieli, 23Abidoni, Zikiri, Hanani, 24Hananiya, Elamu, Anitotiya, 25Ifideya ndi Penueli anali ana a Sasaki.

26Samuserai, Sehariya, Ataliya, 27Yaaresiya, Eliya ndi Zikiri anali ana a Yerohamu.

28Onsewa anali atsogoleri a mabanja, anthu otchuka potsata mibado yawo, ndipo ankakhala mu Yerusalemu.

29Yeiyeli amene amabereka Gibiyoni ankakhala ku Gibiyoni.

Dzina la mkazi wake linali Maaka, 30ndipo mwana wake woyamba anali Abidoni, motsatana ndi Zuri, Kisi, Baala, Neri, Nadabu, 31Gedori, Ahiyo, Zekeri 32ndi Mikiloti, amene anabereka Simea. Iwowa ankakhalanso ku Yerusalemu ndi abale awo.

33Neri anabereka Kisi. Kisi anabereka Sauli, ndipo Sauli anabereka Yonatani, Maliki-Suwa, Abinadabu ndi Esibaala.

34Mwana wa Yonatani anali

Meri-Baala, amene anabereka Mika.

35Ana a Mika anali awa:

Pitoni, Meleki, Tareya ndi Ahazi.

36Ahazi anabereka Yehoyada, Yehoyada anabereka Alemeti, Azimaveti ndi Zimuri, ndipo Zimuri anabereka Moza. 37Moza anabereka Bineya. Ana ake anali Rafa, Eleasa ndi Azeli.

38Azeli anali ndi ana asanu ndi mmodzi, ndipo mayina awo anali awa:

Azirikamu, Bokeru, Ismaeli, Seariya, Obadiya ndi Hanani. Onsewa anali ana a Azeli.

39Ana a Eseki mʼbale wake anali awa:

Mwana wake woyamba Ulamu, wachiwiri Yeusi ndipo wachitatu Elifeleti. 40Ana a Ulamu anali asilikali olimba mtima amene amadziwa kugwiritsa ntchito uta. Iwo anali ndi ana ndi adzukulu ambiri ndipo onse analipo 150.

Onsewa anali adzukulu a Benjamini.