역대상 25 – KLB & CCL

Korean Living Bible

역대상 25:1-31

성가대원들과 그들의 직무

1다윗과 25:1 또는 ‘군대 장관들’레위 지도자들은 아삽과 헤만과 여두둔의 자손 중에서 수금과 비파와 제금에 맞추어 노래로 여호와를 찬양할 사람들을 뽑아 세웠다. 그들의 이름과 그 직무는 다음과 같다:

2삭굴, 요셉, 느다냐, 아사렐라는 그들의 아버지 아삽의 지도를 받아 왕의 명령이 있을 때마다 노래로 하나님의 말씀을 선포하였다.

3그달랴, 스리, 여사야, 하사뱌, 맛디디야는 그들의 아버지 여두둔의 지도를 받아 수금에 맞추어 노래로 하나님의 말씀을 선포하고 여호와께 감사와 찬양을 드렸다.

4-5북기야, 맛다냐, 웃시엘, 스브엘, 여리 못, 하나냐, 하나니, 엘리아다, 깃달디, 로암디 – 에셀, 요스브가사, 말로디, 호딜, 마하시옷은 왕의 예언자 헤만의 아들들이었다. 하나님께서는 헤만에게 이 열네 아들 외에도 딸 셋을 더 주셨다.

6이들은 그 아버지의 지도를 받아 성전에서 제금과 비파와 수금을 타는 사람들이었으며 아삽과 여두둔과 헤만은 왕의 지시를 직접 받는 사람들이었다.

7이상의 사람들과 그들의 친척들은 음악의 전문가로서 여호와를 찬양하는 자들이었는데 이들은 모두 288명이었다.

8이 사람들은 자기들이 맡을 직무를 결정하기 위해서 스승이나 제자나 나이의 많고 적음을 따지지 않고 각 집안별로 제비를 뽑았다. 그리고 각 집안의 구성원은 조장과 그의 아들들과 친척들을 포함하여 모두 12명씩이었다. 제비가 뽑힌 순위와 그 조장들의 이름은 다음과 같다:

9첫째로 뽑힌 사람은 아삽 집안의 요셉, 둘째 그달랴,

10셋째 삭굴,

11넷째 이스리,

12다섯째 느다냐,

13여섯째 북기야,

14일곱째 여사렐라,

15여덟째 여사야,

16아홉째 맛다냐,

17열째 시므이,

18열한째 아사렐,

19열두째 하사뱌,

20열셋째 수바엘,

21열넷째 맛디디야,

22열다섯째 여레못,

23열여섯째 하나냐,

24열일곱째 요스브가사,

25열여덟째 하나니,

26열아홉째 말로디,

27스물째 엘리아다,

28스물한째 호딜,

29스물두째 깃달디,

30스물셋째 마하시옷,

31스물넷째 로암디 – 에셀이었다.

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Mbiri 25:1-31

Anthu Oyimba Nyimbo

1Davide ndi atsogoleri a asilikali anapatula ena mwa ana a Asafu, Hemani ndi Yedutuni ku utumiki wa uneneri pogwiritsa ntchito apangwe, azeze ndi ziwaya zamalipenga. Tsopano nawu mndandanda wa anthu amene ankagwira ntchito imeneyi:

2Kuchokera kwa ana a Asafu:

Zakuri, Yosefe, Netaniya ndi Asareli. Ana a Asafu amalamulidwa ndi Asafu ndipo amanenera moyangʼaniridwa ndi mfumu.

3Kwa Yedutuni, kuchokera kwa ana ake:

Gedaliya, Zeri, Yesaya, Simei, Hasabiya ndi Matitiya. Onse analipo 9 ndipo amayangʼaniridwa ndi Yedutuni abambo awo, amene amanenera pogwiritsa ntchito apangwe poyamika ndi kutamanda Yehova.

4Kwa Hemani, kuchokera kwa ana ake:

Bukiya, Mataniya, Uzieli, Subaeli ndi Yerimoti; Hananiya, Hanani, Eliata, Gidaliti ndi Romamiti-Ezeri; Yosibakasa, Maloti, Hotiri ndi Mahazioti. 5Onsewa anali ana a Hemani mlosi wa mfumu. Iye anapatsidwa anawa potsata mawu a Mulungu akuti adzamukweza. Mulungu anapatsa Hemani ana aamuna 14 ndi ana aakazi atatu.

6Anthu onsewa ankayangʼaniridwa ndi makolo awo pa mayimbidwe a mʼNyumba ya Yehova. Iwowatu ankayimba ndi ziwaya zamalipenga, azeze ndi apangwe potumikira mʼNyumba ya Mulungu. Koma Asafu, Yedutuni ndi Hemani amayangʼaniridwa ndi mfumu. 7Iwo pamodzi ndi abale awo onse ophunzitsidwa ndi aluso loyimbira Yehova chiwerengero chawo chinali 288. 8Angʼonoangʼono ndi akulu omwe, mphunzitsi ndi wophunzira yemwe anachita maere pa ntchito zawo.

9Maere woyamba amene anali a Asafu, anagwera Yosefe,    ana ndi abale ake. 12Maere achiwiri anagwera Gedaliya,    ndi abale ake ndi ana ake. 1210Maere achitatu anagwera Zakuri,    ana ake ndi abale ake.1211Maere achinayi anagwera Iziri,    ana ake ndi abale ake.1212Maere achisanu anagwera Netaniya,    ana ake ndi abale ake.1213Maere achisanu ndi chimodzi anagwera Bukiya,    ana ake ndi abale ake.1214Maere achisanu ndi chiwiri anagwera Yesarela,    ana ake ndi abale ake.1215Maere achisanu ndi chitatu anagwera Yeshaya,    ana ake ndi abale ake.1216Maere achisanu ndi chinayi anagwera Mataniya,    ana ake ndi abale ake.1217Maere a khumi anagwera Simei,    ana ake ndi abale ake.1218Maere a 11 anagwera Azareli,    ana ake ndi abale ake.1219Maere a 12 anagwera Hasabiya,    ana ake ndi abale ake.1220Maere a 13 anagwera Subaeli,    ana ake ndi abale ake.1221Maere a 14 anagwera Matitiya,   ana ake ndi abale ake.1222Maere a 15 anagwera Yeremoti,   ana ake ndi abale ake.1223Maere a 16 anagwera Hananiya,   ana ake ndi abale ake.1224Maere a 17 anagwera Yosibakasa,   ana ake ndi abale ake.1225Maere a 18 anagwera Hanani,   ana ake ndi abale ake.1226Maere a 19 anagwera Maloti,   ana ake ndi abale ake.1227Maere a 20 anagwera Eliyata,   ana ake ndi abale ake.1228Maere a 21 anagwera Hotiri,   ana ake ndi abale ake.1229Maere a 22 anagwera Gidaliti,   ana ake ndi abale ake.1230Maere a 23 anagwera Mahazioti,   ana ake ndi abale ake.1231Maere a 24 anagwera Romamiti-Ezeri,   ana ake ndi abale ake12.