以斯拉記 2 – CCBT & CCL

Chinese Contemporary Bible (Traditional)

以斯拉記 2:1-70

回歸的流亡者名單

1巴比倫尼布甲尼撒從前把猶大省的人擄到巴比倫,這些人的子孫從流亡之地返回耶路撒冷猶大後,各回本城。 2他們是與所羅巴伯耶書亞尼希米西萊雅利來雅末底改必珊米斯拔比革瓦伊利宏巴拿一同回來的。

以下是返回的以色列人的數目:

3巴錄的子孫兩千一百七十二人; 4示法提雅的子孫三百七十二人; 5亞拉的子孫七百七十五人; 6巴哈·摩押的子孫,即耶書亞約押的子孫兩千八百一十二人; 7以攔的子孫一千二百五十四人; 8薩土的子孫九百四十五人; 9薩改的子孫七百六十人; 10巴尼的子孫六百四十二人; 11比拜的子孫六百二十三人; 12押甲的子孫一千二百二十二人; 13亞多尼干的子孫六百六十六人; 14比革瓦伊的子孫兩千零五十六人; 15亞丁的子孫四百五十四人; 16亞特的子孫,即希西迦的子孫九十八人; 17比賽的子孫三百二十三人; 18約拉的子孫一百一十二人; 19哈順的子孫二百二十三人; 20吉罷珥的子孫九十五人。

21伯利恆人一百二十三名; 22尼陀法人五十六名; 23亞拿突人一百二十八名; 24亞斯瑪弗人四十二名; 25基列·耶琳人、基非拉人和比錄人七百四十三名; 26拉瑪人和迦巴人六百二十一名; 27默瑪人一百二十二名; 28伯特利人和人二百二十三名; 29尼波人五十二名; 30末必人一百五十六名; 31另一個以攔的子孫一千二百五十四人; 32哈琳人三百二十名; 33羅德人、哈第人和阿挪人七百二十五名; 34耶利哥人三百四十五名; 35西拿人三千六百三十名。

36祭司有耶大雅的子孫,即耶書亞的子孫九百七十三人; 37音麥的子孫一千零五十二人; 38巴施戶珥的子孫一千二百四十七人; 39哈琳的子孫一千零一十七人。

40利未人有何達威雅的子孫,即耶書亞甲篾的子孫七十四人; 41負責歌樂的亞薩的子孫一百二十八人; 42負責守衛殿門的沙龍的子孫、亞特的子孫、達們的子孫、亞谷的子孫、哈底大的子孫和朔拜的子孫一百三十九人。

43殿役有西哈的子孫、哈蘇巴的子孫、答巴俄的子孫、 44基綠的子孫、西亞的子孫、巴頓的子孫、 45利巴拿的子孫、哈迦巴的子孫、亞谷的子孫、 46哈甲的子孫、薩買的子孫、哈難的子孫、 47吉德的子孫、迦哈的子孫、利亞雅的子孫、 48利汛的子孫、尼哥大的子孫、迦散的子孫、 49烏撒的子孫、巴西亞的子孫、比賽的子孫、 50押拿的子孫、米烏寧的子孫、尼普心的子孫、 51巴卜的子孫、哈古巴的子孫、哈忽的子孫、 52巴洗律的子孫、米希大的子孫、哈沙的子孫、 53巴柯的子孫、西西拉的子孫、答瑪的子孫、 54尼細亞的子孫和哈提法的子孫。

55所羅門僕人的子孫有瑣太的子孫、瑣斐列的子孫、比路大的子孫、 56雅拉的子孫、達昆的子孫、吉德的子孫、 57示法提雅的子孫、哈替的子孫、玻黑列·哈斯巴音的子孫和亞米的子孫。

58殿役和所羅門僕人的子孫共三百九十二人。

59以下這些人來自特·米拉特·哈薩基綠押但音麥,但不能證明自己是以色列人的後代: 60第來雅的子孫、多比雅的子孫和尼哥大的子孫,共六百五十二人。

61-62祭司中的哈巴雅宗族、哈哥斯宗族和巴西萊宗族,在族譜中都找不到自己的譜系,因此他們算為不潔淨,不能做祭司。巴西萊子孫的祖先娶了基列巴西萊的女兒為妻,因此取名叫巴西萊63省長吩咐他們,要等到用烏陵和土明求問上帝的祭司出現後,才可以吃至聖之物。

64回到猶大的人共四萬二千三百六十名。 65此外還有他們的七千三百三十七名男女僕婢,二百名男女歌樂手, 66七百三十六匹馬,二百四十五匹騾子, 67四百三十五頭駱駝和六千七百二十頭驢。

68有些族長來到耶路撒冷耶和華的殿時,甘願為上帝的殿獻上禮物,用來在舊址上重新建殿。 69他們盡自己的能力為這工程捐獻了五百公斤金子,三噸銀子,以及一百件祭司禮服。

70祭司、利未人、一些百姓、歌樂手、殿門守衛和殿役住在自己的城裡,其餘的以色列人也都住在自己的城裡。

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

Ezara 2:1-70

Mʼndandanda wa Ayuda amene Anabwerera

1Awa ndi anthu a mʼchigawo cha Yuda amene anabwerako ku ukapolo, amene Nebukadinezara mfumu ya ku Babuloni anawagwira ukapolo ndi kupita nawo ku Babuloni (iwo anabwerera ku Yerusalemu ndi ku Yuda, aliyense ku mzinda wake. 2Iwo anabwerera pamodzi ndi Zerubabeli, Yesuwa, Nehemiya, Seruya, Reelaya, Mordekai, Bilisani, Misipara, Bigivai, Rehumu ndi Baana).

Chiwerengero cha anthu aamuna a Israeli chinali chotere:

3Zidzukulu za Parosi 2,1724zidzukulu za Sefatiya 3725zidzukulu za Ara 7756zidzukulu za Pahati-Mowabu (zochokera kwa Yesuwa ndi Yowabu) 2,8127zidzukulu za Elamu 1,2548zidzukulu za Zatu 9459zidzukulu za Zakai 76010zidzukulu za Bani 64211zidzukulu za Bebai 62312zidzukulu za Azigadi 1,22213zidzukulu za Adonikamu 66614zidzukulu za Bigivai 2,05615zidzukulu za Adini 45416zidzukulu za Ateri (kudzera mwa Hezekiya) 9817zidzukulu za Bezayi 32318zidzukulu za Yora 11219zidzukulu za Hasumu 22320zidzukulu za Gibari 95.

21Anthu a ku Betelehemu 12322Anthu aamuna a ku Netofa 5623Anthu aamuna a ku Anatoti 12824Anthu aamuna a ku Azimaveti 4225Anthu aamuna a ku Kiriati Yearimu, Kefira ndi Beeroti 74326Anthu aamuna a ku Rama ndi Geba 62127Anthu aamuna a ku Mikimasi 12228Anthu aamuna a ku Beteli ndi Ai 22329Anthu aamuna a ku Nebo 5230Anthu aamuna a ku Magaibisi 15631Anthu aamuna a ku Elamu wina 1,25432Anthu aamuna a ku Harimu 32033Anthu aamuna a ku Lodi, Hadidi ndi Ono 72534Anthu aamuna a ku Yeriko 34535Anthu aamuna a ku Sena 3,630.

36Ansembe anali awa:

   Zidzukulu za Yedaya (kudzera mu banja la Yesuwa) 97337Zidzukulu za Imeri 1,05238Zidzukulu za Pasuri 1,24739Zidzukulu za Harimu 1,017.

40Alevi anali awa:

   Zidzukulu za Yesuwa ndi Kadimieli (kudzera mwa ana a Hodaviya) 74.

41Anthu oyimba nyimbo anali awa:

   Zidzukulu za Asafu 128.

42Alonda a ku Nyumba ya Mulungu anali awa:

   Zidzukulu za Salumu, zidzukulu za Ateri, zidzukulu za Talimoni, zidzukulu za Akubu, zidzukulu za Hatita ndi zidzukulu za Sobai 139.

43Otumikira ku Nyumba ya Mulungu anali awa:

Zidzukulu za   Ziha, zidzukulu za Hasufa, zidzukulu za Tabaoti,44zidzukulu za Kerosi, zidzukulu za Siyaha, Padoni,45zidzukulu za Lebana, zidzukulu za Hagaba, zidzukulu za Akubu,46zidzukulu za Hagabu, zidzukulu za Salimayi, zidzukulu za Hanani,47zidzukulu za Gideli, zidzukulu za Gahari, zidzukulu za Reaya,48zidzukulu za Rezini, zidzukulu za Nekoda, zidzukulu za Gazamu,49zidzukulu za Uza, zidzukulu za Peseya, zidzukulu za Besai,50zidzukulu za Asina, zidzukulu za Meunimu, Nefusimu,51zidzukulu za Bakibuku, zidzukulu za Hakufa, zidzukulu za Harihuri,52zidzukulu za Baziruti, zidzukulu za Mehida, zidzukulu za Harisa,53zidzukulu za Barikosi, zidzukulu za Sisera, zidzukulu za Tema,54zidzukulu za Neziya ndi zidzukulu za Hatifa.

55Zidzukulu za antchito a Solomoni zinali izi:

Zidzukulu za   Sotai, zidzukulu za Hasofereti, zidzukulu za Peruda,56zidzukulu za Yaala, zidzukulu za Darikoni, zidzukulu za Gideli,57zidzukulu za Sefatiya, zidzukulu za Hatilu,   zidzukulu za Pokereti, Hazebayimu ndi Ami.58Chiwerengero cha onse otumikira ku Nyumba ya Mulungu pamodzi ndi zidzukulu za Solomoni chinali 392.

59Anthu ali mʼmunsiwa anabwera kuchokera ku mizinda ya Teli-Mela, Teli-Harisa, Kerubi, Adoni ndi Imeri, ngakhale samatha kutsimikiza kuti mafuko awo analidi Aisraeli enieni kapena ayi:

60Zidzukulu za Delaya, zidzukulu za Tobiya, ndi zidzukulu za Nekoda. Onse pamodzi anali 652.

61Ndi ena pakati pa ansembe anali awa:

Zidzukulu za   Hobiya, Hakozi, ndi Barizilai (Zidzukulu za Hobiya, zidzukulu za Hakozi ndi zidzukulu za Barizilai. Barizilai ameneyu ndi uja anakwatira mmodzi mwa ana aakazi a Barizilai Mgiliyadi ndipo ankadziwika ndi dzina la bambo wawoyo.)

62Amenewa anafufuza mayina awo mʼbuku lofotokoza mbiri ya mafuko awo, koma mayinawo sanawapezemo, choncho anawachotsa pa unsembe ngati anthu odetsedwa pa zachipembedzo. 63Bwanamkubwa anawawuza anthuwo kuti asamadye nawo mpaka atapezeka wansembe wodziwa kuwombeza ndi Urimu ndi Tumimu.

64Chiwerengero cha anthu onse pamodzi chinali 42,360, 65kuwonjezera pamenepo, panalinso antchito awo aamuna ndi aakazi okwanira 7,337. Analinso ndi amuna ndi akazi oyimba nyimbo okwanira 200. 66Anali ndi akavalo 736, nyulu 245, 67ngamira 435 ndi abulu 6,720.

68Atafika ku Nyumba ya Yehova mu Yerusalemu, ena mwa atsogoleri a mabanja anapereka zopereka zaufulu zothandizira kumanganso Nyumba ya Mulungu pamalo pake pakale. 69Anapereka kwa msungichuma wa ntchitoyo molingana ndi mmene aliyense chuma chake chinalili: golide wa makilogalamu 500, siliva makilogalamu 2,800 ndi zovala za ansembe zokwanira 100.

70Ansembe, Alevi, oyimba nyimbo, alonda ndi antchito a ku Nyumba ya Yehova pamodzi ndi Aisraeli ena onse ankakhala mʼmidzi ya makolo awo.